Views : 3,186
Genre: People & Blogs
Date of upload: Apr 27, 2024 ^^
Rating : 5 (0/50 LTDR)
RYD date created : 2024-04-27T14:39:23.475623Z
See in json
Top Comments of this video!! :3
Amalawi zonse tikuona zipani zoyambika CHIFUKWA CHA nkwiyo tikuziziwa osadandaula ayi ife tikavotera dpp basi komaso chakwera asaiwale mau amene ananena oti azakhesa mwazi chakwera akazangowina 2025 anthu sitizalola ai chakwera wazunza Amalawi kwambiri ππππππAmalawi tisagone ai tipemphere zolimba kwambiri kuti Satan ameneyi achoke basi πππ
4 |
@user-vl8uw8mc3u
2 weeks ago
Nankhumwa ndi mwana.akulephela kupeza dzina la chipani chawoππππππππ
1 |