Ngati Muli ndi Maganizo kapena mukufuna kuwadziwitsa anthu zomwe mumapanga tilembeleni pa dziwetv@yahoo.com
Dziwetv ndi Channel Yomwe makamaka ikuyang'ana kwambiri nkhani Zandale Mdziko lino. Kuwadziwitsa anthu zomwe Mtsogoleri wadziko lino walankhula ndi azitsogoleri ena azipani zina. Dziwe simalimbikitsa Ulamuliro wankhanza ndipo timapanga Support ulamuliro Osamala Malamulo.
Anthu omwe alibe information zomwe zikuchitika mdziko mwawo ndi anthu omwe ali otayika.